Deuteronomo 33:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Ndiwe wosangalala iwe Isiraeli!+ Ndani angafanane ndi iwe,+Anthu amene akupulumutsidwa ndi Yehova,+Chishango chako chokuteteza,+Komanso lupanga lako lamphamvu? Adani ako adzakhala mwamantha chifukwa cha iwe,+Ndipo iwe udzaponda pamisana yawo.”* Miyambo 30:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mawu onse a Mulungu ndi oyengeka.+ Iye ndi chishango kwa onse amene amathawira kwa iye.+
29 Ndiwe wosangalala iwe Isiraeli!+ Ndani angafanane ndi iwe,+Anthu amene akupulumutsidwa ndi Yehova,+Chishango chako chokuteteza,+Komanso lupanga lako lamphamvu? Adani ako adzakhala mwamantha chifukwa cha iwe,+Ndipo iwe udzaponda pamisana yawo.”*