1 Akorinto 15:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Paja Malemba amati: “Adamu, yemwe anali munthu woyambirira, anakhala munthu wamoyo.”+ Adamu womalizira anakhala mzimu wopatsa moyo.+ 1 Akorinto 15:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Munthu woyambayo anachokera padziko lapansi ndipo anapangidwa ndi dothi.*+ Wachiwiriyo anachokera kumwamba.+
45 Paja Malemba amati: “Adamu, yemwe anali munthu woyambirira, anakhala munthu wamoyo.”+ Adamu womalizira anakhala mzimu wopatsa moyo.+
47 Munthu woyambayo anachokera padziko lapansi ndipo anapangidwa ndi dothi.*+ Wachiwiriyo anachokera kumwamba.+