Genesis 18:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Atakweza maso, anaona amuna atatu ataima chapatali ndi iye.+ Atawaona, ananyamuka pakhomo la tentiyo nʼkuthamanga kukakumana nawo. Atafika, anagwada nʼkuwerama mpaka nkhope yake pansi. Genesis 18:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Kenako amunawo anachoka pamalowo nʼkulowera ku Sodomu, koma Yehova+ anatsala ndi Abulahamu.
2 Atakweza maso, anaona amuna atatu ataima chapatali ndi iye.+ Atawaona, ananyamuka pakhomo la tentiyo nʼkuthamanga kukakumana nawo. Atafika, anagwada nʼkuwerama mpaka nkhope yake pansi.