Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 29:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 akadzaona kuti dziko lonse lawonongedwa ndi sulufule, mchere ndi kutentha, moti mʼdzikomo simungadzalidwe mbewu, simungaphuke kalikonse ndipo simungamere chomera chilichonse, ndipo likuoneka ngati Sodomu ndi Gomora,+ Adima ndi Zeboyimu,+ mizinda imene Yehova anaiwononga ndi ukali komanso mkwiyo wake—*

  • Luka 17:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Koma tsiku limene Loti anatuluka mu Sodomu, kumwamba kunagwa moto ndi sulufule ngati mvula nʼkuwononga anthu onse.+

  • 2 Petulo 2:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Anawononganso mizinda ya Sodomu ndi Gomora poitentha ndi moto.+ Anachita zimenezi kuti likhale chenjezo kwa anthu osaopa Mulungu la zimene zidzawachitikire mʼtsogolo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena