Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 2:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Mukafika pafupi ndi Aamoni, musawavutitse kapena kulimbana nawo, chifukwa sindidzakupatsani mbali iliyonse ya dziko la Aamoni kuti likhale lanu. Dziko limeneli ndinalipereka kwa mbadwa za Loti kuti likhale lawo.+

  • Oweruza 11:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Patapita nthawi, Aamoni anayamba kumenyana ndi Aisiraeli.+

  • Nehemiya 13:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Pa tsiku limenelo buku la Mose linawerengedwa anthu onse akumva.+ Iwo anapeza kuti mʼbukumo analembamo kuti mbadwa iliyonse ya Amoni ndi ya Mowabu+ isamaloledwe kukhala mʼgulu la anthu a Mulungu woona,+

  • Zefaniya 2:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  9 Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, Mulungu wa Isiraeli wanena kuti: “Pali ine Mulungu wamoyo,

      Mowabu adzakhala ngati Sodomu,+

      Ndipo Amoni adzakhala ngati Gomora,+

      Malo okhala ndi zomera zoyabwa, dothi lamchere ndiponso malo abwinja mpaka kalekale.+

      Anthu anga amene adzatsale adzatenga zinthu za anthu amenewa,

      Ndipo anthu amtundu wanga amene adzatsale, adzawalanda anthuwa zinthu zawo.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena