Genesis 17:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndiyeno Mulungu anati: “Ndithu Sara mkazi wako adzakuberekera mwana wamwamuna ndipo udzamʼpatse dzina lakuti Isaki.*+ Ndidzakhazikitsa pangano ndi iye, kuti likhale pangano losatha kwa mbadwa zake.+ Yoswa 24:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Patapita nthawi, ndinatenga kholo lanu Abulahamu+ kuchokera kutsidya lina la Mtsinje.* Ndinamuyendetsa mʼdziko lonse la Kanani ndipo ndinachulukitsa mbadwa zake.*+ Ndinamʼpatsa Isaki+ Aroma 9:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndiponso sikuti onse ndi ana chifukwa choti ndi mbadwa* za Abulahamu.+ Koma Malemba amati, “Mbadwa* zimene ndinakulonjeza zidzachokera mwa Isaki.”+
19 Ndiyeno Mulungu anati: “Ndithu Sara mkazi wako adzakuberekera mwana wamwamuna ndipo udzamʼpatse dzina lakuti Isaki.*+ Ndidzakhazikitsa pangano ndi iye, kuti likhale pangano losatha kwa mbadwa zake.+
3 Patapita nthawi, ndinatenga kholo lanu Abulahamu+ kuchokera kutsidya lina la Mtsinje.* Ndinamuyendetsa mʼdziko lonse la Kanani ndipo ndinachulukitsa mbadwa zake.*+ Ndinamʼpatsa Isaki+
7 Ndiponso sikuti onse ndi ana chifukwa choti ndi mbadwa* za Abulahamu.+ Koma Malemba amati, “Mbadwa* zimene ndinakulonjeza zidzachokera mwa Isaki.”+