Genesis 15:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndiyeno Mulungu anauza Abulamu kuti: “Udziwe ndithu kuti mbadwa* zako zidzakhala alendo mʼdziko la eni ndipo anthu adzazisandutsa akapolo ndi kuzizunza kwa zaka 400.+ Agalatiya 4:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Mwachitsanzo, Malemba amanena kuti Abulahamu anabereka ana aamuna awiri, wina kwa kapolo wamkazi+ ndipo wina kwa mkazi amene anali mfulu.+ Agalatiya 4:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Koma mofanana ndi mmene zinalili pa nthawiyo, kuti amene anabadwa ngati mmene ana onse amabadwira anayamba kuzunza amene anabadwa kudzera mwa mzimu,+ ndi mmenenso zilili masiku ano.+
13 Ndiyeno Mulungu anauza Abulamu kuti: “Udziwe ndithu kuti mbadwa* zako zidzakhala alendo mʼdziko la eni ndipo anthu adzazisandutsa akapolo ndi kuzizunza kwa zaka 400.+
22 Mwachitsanzo, Malemba amanena kuti Abulahamu anabereka ana aamuna awiri, wina kwa kapolo wamkazi+ ndipo wina kwa mkazi amene anali mfulu.+
29 Koma mofanana ndi mmene zinalili pa nthawiyo, kuti amene anabadwa ngati mmene ana onse amabadwira anayamba kuzunza amene anabadwa kudzera mwa mzimu,+ ndi mmenenso zilili masiku ano.+