Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 17:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Ndiyeno Mulungu anati: “Ndithu Sara mkazi wako adzakuberekera mwana wamwamuna ndipo udzamʼpatse dzina lakuti Isaki.*+ Ndidzakhazikitsa pangano ndi iye, kuti likhale pangano losatha kwa mbadwa zake.+

  • Aroma 9:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Ndiponso sikuti onse ndi ana chifukwa choti ndi mbadwa* za Abulahamu.+ Koma Malemba amati, “Mbadwa* zimene ndinakulonjeza zidzachokera mwa Isaki.”+

  • Aheberi 11:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Anali wokonzeka kuchita zimenezo ngakhale kuti anali atauzidwa kuti: “Mbadwa* zimene ndinakulonjeza zidzachokera mwa Isaki.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena