Genesis 25:5, 6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pambuyo pake, Abulahamu anapatsa Isaki zonse zimene anali nazo.+ 6 Koma Abulahamu anapereka mphatso kwa ana amene adzakazi ake anamuberekera. Kenako, iye adakali ndi moyo, anatumiza anawo Kumʼmawa, kutali ndi mwana wake Isaki.+
5 Pambuyo pake, Abulahamu anapatsa Isaki zonse zimene anali nazo.+ 6 Koma Abulahamu anapereka mphatso kwa ana amene adzakazi ake anamuberekera. Kenako, iye adakali ndi moyo, anatumiza anawo Kumʼmawa, kutali ndi mwana wake Isaki.+