1 Akorinto 11:8, 9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Chifukwa mwamuna sanachokere kwa mkazi, koma mkazi anachokera kwa mwamuna.+ 9 Ndiponso mwamuna sanalengedwere mkazi, koma mkazi analengedwera mwamuna.+ 1 Timoteyo 2:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Chifukwa Adamu ndi amene anayamba kupangidwa kenako Hava.+
8 Chifukwa mwamuna sanachokere kwa mkazi, koma mkazi anachokera kwa mwamuna.+ 9 Ndiponso mwamuna sanalengedwere mkazi, koma mkazi analengedwera mwamuna.+