Genesis 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Atatero onse maso awo anatseguka ndipo anazindikira kuti ali maliseche. Choncho anasoka masamba a mkuyu nʼkuwamangirira mʼchiuno mwawo.+
7 Atatero onse maso awo anatseguka ndipo anazindikira kuti ali maliseche. Choncho anasoka masamba a mkuyu nʼkuwamangirira mʼchiuno mwawo.+