2 Akorinto 11:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mofanana ndi mmene njoka inanamizira Hava ndi chinyengo chake,+ nkhawa yanga ndi yakuti mwina maganizo anunso angapotozedwe moti simungakhalenso oona mtima ndiponso oyera. Koma munthu wa Khristu amafunika kukhala woona mtima komanso woyera.+ 1 Timoteyo 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Komanso Adamu sanapusitsidwe, koma mkaziyo ndi amene anapusitsidwa+ ndipo anachimwa. Yakobo 1:14, 15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma munthu aliyense amayesedwa ndi chilakolako chake chimene chimamukopa* ndi kumukola.+ 15 Ndiye chilakolako chikatenga pakati, chimabereka tchimo. Ndipo tchimo likachitika, limabweretsa imfa.+
3 Mofanana ndi mmene njoka inanamizira Hava ndi chinyengo chake,+ nkhawa yanga ndi yakuti mwina maganizo anunso angapotozedwe moti simungakhalenso oona mtima ndiponso oyera. Koma munthu wa Khristu amafunika kukhala woona mtima komanso woyera.+
14 Koma munthu aliyense amayesedwa ndi chilakolako chake chimene chimamukopa* ndi kumukola.+ 15 Ndiye chilakolako chikatenga pakati, chimabereka tchimo. Ndipo tchimo likachitika, limabweretsa imfa.+