Chivumbulutso 20:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kenako anagwira chinjoka,+ njoka yakale ija,+ amene ndi Mdyerekezi+ ndiponso Satana,+ nʼkumumanga kwa zaka 1,000. Chivumbulutso 20:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mdyerekezi, amene ankawasocheretsa, adzaponyedwa mʼnyanja yamoto ndi sulufule, mmene muli kale chilombo+ ndi mneneri wabodza uja.+ Ndipo iwo adzazunzidwa masana ndi usiku* mpaka kalekale.
2 Kenako anagwira chinjoka,+ njoka yakale ija,+ amene ndi Mdyerekezi+ ndiponso Satana,+ nʼkumumanga kwa zaka 1,000.
10 Mdyerekezi, amene ankawasocheretsa, adzaponyedwa mʼnyanja yamoto ndi sulufule, mmene muli kale chilombo+ ndi mneneri wabodza uja.+ Ndipo iwo adzazunzidwa masana ndi usiku* mpaka kalekale.