Genesis 29:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Yehova ataona kuti Leya sankakondedwa kwenikweni,* anamʼpatsa mphamvu zobereka,*+ koma Rakele anali wosabereka.+
31 Yehova ataona kuti Leya sankakondedwa kwenikweni,* anamʼpatsa mphamvu zobereka,*+ koma Rakele anali wosabereka.+