-
Genesis 30:32Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
32 Ine ndipita kukayenda pakati pa ziweto zanu zonse lero. Inuyo mukapatule nkhosa iliyonse yamathothomathotho kapena yamawangamawanga, ndi nkhosa iliyonse yaingʼono yamphongo yabulauni, ndi mbuzi iliyonse yaikazi yamawangamawanga kapena yamathothomathotho. Kuyambira panopa, ziweto zimene zizibadwa motere zizikhala malipiro anga.+
-