Genesis 35:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Zitatero, Yakobo anaimika mwala wachikumbutso pamalo amene ankalankhula nayepo, kenako pamwalawo anathirapo nsembe yachakumwa ndi mafuta.+ Genesis 37:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Yakobo anapitiriza kukhala mʼdziko la Kanani, kumene bambo ake anakhalako ngati mlendo.+
14 Zitatero, Yakobo anaimika mwala wachikumbutso pamalo amene ankalankhula nayepo, kenako pamwalawo anathirapo nsembe yachakumwa ndi mafuta.+