Genesis 31:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kenako Yehova anauza Yakobo kuti: “Bwerera kudziko la makolo ako ndi kwa abale ako,+ ndipo ine ndidzapitiriza kukuthandiza.”
3 Kenako Yehova anauza Yakobo kuti: “Bwerera kudziko la makolo ako ndi kwa abale ako,+ ndipo ine ndidzapitiriza kukuthandiza.”