Genesis 20:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pambuyo pake Mulungu anafikira Abimeleki usiku mʼmaloto nʼkumuuza kuti: “Ufatu iwe chifukwa mkazi amene watengayu+ ndi wokwatiwa.”+
3 Pambuyo pake Mulungu anafikira Abimeleki usiku mʼmaloto nʼkumuuza kuti: “Ufatu iwe chifukwa mkazi amene watengayu+ ndi wokwatiwa.”+