Genesis 25:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Isaki anali ndi zaka 40 pamene anakwatira Rabeka, mwana wa Betuele+ wa Chiaramu, wa ku Padani-aramu, amene anali mchemwali wake wa Labani wa Chiaramu. Hoseya 12:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Yakobo anathawira mʼdera la Aramu.*+Ndipo Isiraeli+ ankagwira ntchito kumeneko kuti apeze mkazi,+Ankalondera nkhosa kuti apeze mkazi.+
20 Isaki anali ndi zaka 40 pamene anakwatira Rabeka, mwana wa Betuele+ wa Chiaramu, wa ku Padani-aramu, amene anali mchemwali wake wa Labani wa Chiaramu.
12 Yakobo anathawira mʼdera la Aramu.*+Ndipo Isiraeli+ ankagwira ntchito kumeneko kuti apeze mkazi,+Ankalondera nkhosa kuti apeze mkazi.+