-
Genesis 46:25Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
25 Amenewa ndi ana a Biliha, yemwe Labani anamupereka kwa mwana wake wamkazi Rakele. Iye anaberekera Yakobo ana amenewa. Onse pamodzi analipo 7.
-