-
Genesis 31:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Koma bambo anu akhala akundipusitsa, ndipo asintha malipiro anga maulendo 10. Ngakhale zili choncho, Mulungu sanawalole kuti andichitire zoipa.
-