-
Genesis 17:1Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Abulamu ali ndi zaka 99, Yehova anaonekera kwa iye nʼkumuuza kuti: “Ine ndine Mulungu Wamphamvuyonse. Uziyenda mʼnjira zanga ndipo ukhale wopanda cholakwa.
-