-
Genesis 24:59, 60Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
59 Choncho iwo analola kuti mchemwali wawo Rabeka+ ndi mlezi* wake,+ apite limodzi ndi mtumiki wa Abulahamuyo ndi anyamata ake. 60 Ndiyeno iwo anadalitsa Rabeka kuti: “Iwe mchemwali wathu, ukakhale mayi wa anthu masauzande kuchulukitsa ndi masauzande 10, ndipo mbadwa* zako zikalande mizinda ya adani awo.”+
-