Genesis 30:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Yakobo anapeza chuma chambiri. Iye anali ndi ziweto zambiri, antchito aakazi ndi aamuna komanso ngamila ndi abulu.+
43 Yakobo anapeza chuma chambiri. Iye anali ndi ziweto zambiri, antchito aakazi ndi aamuna komanso ngamila ndi abulu.+