Genesis 33:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Tsopano Esau anafunsa kuti: “Nanga nʼchifukwa chiyani watumiza magulu onse amene ndakumana nawo aja?”+ Iye anayankha kuti: “Ndachita zimenezi kuti mundikomere mtima mbuyanga.”+
8 Tsopano Esau anafunsa kuti: “Nanga nʼchifukwa chiyani watumiza magulu onse amene ndakumana nawo aja?”+ Iye anayankha kuti: “Ndachita zimenezi kuti mundikomere mtima mbuyanga.”+