Genesis 30:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kenako Rakele anati: “Tengani kapolo wanga Biliha+ kuti mugone naye nʼcholinga choti andiberekere ana,* kuti inenso ndikhale ndi ana kudzera mwa iye.” Genesis 30:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Leya ataona kuti wasiya kubereka, anapereka kapolo wake Zilipa kwa Yakobo kuti akhale mkazi wake.+
3 Kenako Rakele anati: “Tengani kapolo wanga Biliha+ kuti mugone naye nʼcholinga choti andiberekere ana,* kuti inenso ndikhale ndi ana kudzera mwa iye.”