Hoseya 12:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Anapitiriza kulimbana ndi mngelo ndipo anapambana. Analira komanso anachonderera kuti amudalitse.”+ Mulungu anamupeza ku Beteli ndipo kumeneko Mulungu analankhula nafe.*+
4 Anapitiriza kulimbana ndi mngelo ndipo anapambana. Analira komanso anachonderera kuti amudalitse.”+ Mulungu anamupeza ku Beteli ndipo kumeneko Mulungu analankhula nafe.*+