Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 26:34, 35
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 34 Esau atakwanitsa zaka 40, anakwatira Yuditi mwana wa Beeri, Muhiti. Anakwatiranso Basemati mwana wa Eloni, Muhiti.+ 35 Akaziwo anabweretsa chisoni kwa Isaki ndi Rabeka.+

  • Genesis 27:46
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 46 Izi zitachitika, Rabeka ankauza Isaki nthawi ndi nthawi kuti: “Moyo wanga ndikunyansidwa nawo chifukwa cha akazi a Chihetiwa.+ Ngati Yakobo nayenso angatenge mkazi pakati pa akazi a Chiheti ngati amenewa, ndi bwino ndingofa!”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena