Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 24:2, 3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Ndiyeno Abulahamu anauza mtumiki wake, yemwe anali wamkulu kwambiri mʼnyumba yake komanso woyangʼanira zinthu zake zonse+ kuti: “Chonde, ika dzanja lako pansi pa ntchafu yanga. 3 Ndikufuna ulumbire pali Yehova, Mulungu wakumwamba ndi Mulungu wa dziko lapansi, kuti sutengera mwana wanga mkazi pakati pa ana aakazi a Akanani, amene ndikukhala mʼdziko lawo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena