Genesis 34:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Tikulolani pokhapokha ngati mwamuna aliyense atadulidwa+ kuti mukhale ofanana ndi ife.