Salimo 105:17, 18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mulungu anatsogoza Yosefe,Munthu amene anagulitsidwa kuti akhale kapolo.+ 18 Kumeneko anamanga* mapazi ake mʼmatangadza,+Khosi lake analiika mʼzitsulo
17 Mulungu anatsogoza Yosefe,Munthu amene anagulitsidwa kuti akhale kapolo.+ 18 Kumeneko anamanga* mapazi ake mʼmatangadza,+Khosi lake analiika mʼzitsulo