Ekisodo 2:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Patapita nthawi yaitali mfumu ya Iguputo inamwalira.+ Koma Aisiraeli anapitirizabe kuvutika chifukwa cha ukapolo ndipo ankalira modandaula. Iwo anapitirizabe kulirira Mulungu woona+ kuti awathandize chifukwa cha ukapolowo. Machitidwe 7:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndipo Mulungu anamuuzanso kuti mbadwa* zake zidzakhala alendo mʼdziko la eni, ndipo anthu adzawasandutsa akapolo ndi kuwazunza kwa zaka 400.+
23 Patapita nthawi yaitali mfumu ya Iguputo inamwalira.+ Koma Aisiraeli anapitirizabe kuvutika chifukwa cha ukapolo ndipo ankalira modandaula. Iwo anapitirizabe kulirira Mulungu woona+ kuti awathandize chifukwa cha ukapolowo.
6 Ndipo Mulungu anamuuzanso kuti mbadwa* zake zidzakhala alendo mʼdziko la eni, ndipo anthu adzawasandutsa akapolo ndi kuwazunza kwa zaka 400.+