-
Ezekieli 16:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Pa tsiku limene unabadwa, mchombo wako sunadulidwe. Sanakusambitse kuti ukhale woyera, sanakupake mchere ndipo sanakukulunge munsalu.
-