Ekisodo 7:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pamenepo Aiguputo adzadziwa kuti ine ndine Yehova+ ndikadzatambasula dzanja langa ndi kulanga Iguputo, nʼkutulutsa Aisiraeli mʼdzikolo.” Ekisodo 8:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Pa tsiku limenelo ndidzapatula dera la Goseni kumene kuli anthu anga. Kumeneko sikudzakhala ntchentche zoluma.+ Ndidzachita zimenezi kuti udziwe kuti ine Yehova, ndili mʼdziko lino.+
5 Pamenepo Aiguputo adzadziwa kuti ine ndine Yehova+ ndikadzatambasula dzanja langa ndi kulanga Iguputo, nʼkutulutsa Aisiraeli mʼdzikolo.”
22 Pa tsiku limenelo ndidzapatula dera la Goseni kumene kuli anthu anga. Kumeneko sikudzakhala ntchentche zoluma.+ Ndidzachita zimenezi kuti udziwe kuti ine Yehova, ndili mʼdziko lino.+