2 Mbiri 20:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ulendo uno simufunikira kumenya nkhondo. Aliyense angoima pamalo ake+ nʼkuona mmene Yehova angakupulumutsireni.+ Inu Ayuda ndi anthu a ku Yerusalemu, musaope kapena kuchita mantha.+ Mawa mupite kukakumana nawo ndipo Yehova akhala nanu.’”+
17 Ulendo uno simufunikira kumenya nkhondo. Aliyense angoima pamalo ake+ nʼkuona mmene Yehova angakupulumutsireni.+ Inu Ayuda ndi anthu a ku Yerusalemu, musaope kapena kuchita mantha.+ Mawa mupite kukakumana nawo ndipo Yehova akhala nanu.’”+