Deuteronomo 1:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Yehova Mulungu wanu adzakutsogolerani ndipo adzakumenyerani nkhondo,+ ngati mmene anachitira ku Iguputo inu mukuona.+ Deuteronomo 20:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 chifukwa Yehova Mulungu wanu akuyenda nanu limodzi kuti akumenyereni nkhondo nʼkukupulumutsani kwa adani anu.’+ 2 Mbiri 20:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Maufumu onse amʼdzikolo atamva kuti Yehova wagonjetsa adani a Isiraeli, anakhala ndi mantha ochokera kwa Mulungu.+
30 Yehova Mulungu wanu adzakutsogolerani ndipo adzakumenyerani nkhondo,+ ngati mmene anachitira ku Iguputo inu mukuona.+
4 chifukwa Yehova Mulungu wanu akuyenda nanu limodzi kuti akumenyereni nkhondo nʼkukupulumutsani kwa adani anu.’+
29 Maufumu onse amʼdzikolo atamva kuti Yehova wagonjetsa adani a Isiraeli, anakhala ndi mantha ochokera kwa Mulungu.+