Salimo 105:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Mulungu anatumiza mtambo kuti uwateteze+ Komanso moto kuti uziwaunikira usiku.+