1 Akorinto 10:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Tsopano abale, ndikufuna mudziwe kuti makolo athu akale, onse anali pansi pa mtambo+ ndipo onse anawoloka nyanja.+ Aheberi 11:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Chifukwa cha chikhulupiriro, anthu a Mulunguwo anawoloka pa Nyanja Yofiira patauma ngati pamtunda,+ koma Aiguputo atayesa kudutsa, nyanjayo inawamiza.+
10 Tsopano abale, ndikufuna mudziwe kuti makolo athu akale, onse anali pansi pa mtambo+ ndipo onse anawoloka nyanja.+
29 Chifukwa cha chikhulupiriro, anthu a Mulunguwo anawoloka pa Nyanja Yofiira patauma ngati pamtunda,+ koma Aiguputo atayesa kudutsa, nyanjayo inawamiza.+