Ekisodo 15:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Pamene amuna ankaimba, Miriamu ankathirira mangʼombe kuti: “Imbirani Yehova chifukwa walemekezeka kwambiri.+ Mahatchi ndi okwera pamahatchiwo wawaponyera mʼnyanja.”+ Salimo 136:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Anakutumulira Farao ndi asilikali ake mʼNyanja Yofiira,+Chifukwa chikondi chake chokhulupirika chidzakhalapo mpaka kalekale.
21 Pamene amuna ankaimba, Miriamu ankathirira mangʼombe kuti: “Imbirani Yehova chifukwa walemekezeka kwambiri.+ Mahatchi ndi okwera pamahatchiwo wawaponyera mʼnyanja.”+
15 Anakutumulira Farao ndi asilikali ake mʼNyanja Yofiira,+Chifukwa chikondi chake chokhulupirika chidzakhalapo mpaka kalekale.