Ekisodo 6:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndinkaonekera kwa Abulahamu, Isaki ndi Yakobo monga Mulungu Wamphamvuyonse.+ Koma za dzina langa lakuti Yehova,+ ine sindinadzidziwikitse kwa iwo.+ Yesaya 42:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ine ndine Yehova. Dzina langa ndi limeneli.Sindipereka ulemerero wanga kwa wina aliyenseNdipo sindifuna kuti aliyense azitamanda zifaniziro zogoba mʼmalo mwa ine.+
3 Ndinkaonekera kwa Abulahamu, Isaki ndi Yakobo monga Mulungu Wamphamvuyonse.+ Koma za dzina langa lakuti Yehova,+ ine sindinadzidziwikitse kwa iwo.+
8 Ine ndine Yehova. Dzina langa ndi limeneli.Sindipereka ulemerero wanga kwa wina aliyenseNdipo sindifuna kuti aliyense azitamanda zifaniziro zogoba mʼmalo mwa ine.+