Ekisodo 14:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Nthawi yomweyo Mose anatambasula dzanja lake nʼkuloza panyanja, ndipo kutatsala pangʼono kucha nyanjayo inayamba kubwerera mʼmalo mwake. Pamene Aiguputo ankathawa kuti madziwo asawapeze, Yehova anakankhira Aiguputowo pakatikati pa nyanja.+
27 Nthawi yomweyo Mose anatambasula dzanja lake nʼkuloza panyanja, ndipo kutatsala pangʼono kucha nyanjayo inayamba kubwerera mʼmalo mwake. Pamene Aiguputo ankathawa kuti madziwo asawapeze, Yehova anakankhira Aiguputowo pakatikati pa nyanja.+