Yesaya 37:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Kodi ndi ndani amene iwe wamutonza+ ndi kumunyoza? Ndi ndani amene iwe wamulankhula mokweza,+Ndiponso kumukwezera maso ako onyada? Ndi Woyera wa Isiraeli!+
23 Kodi ndi ndani amene iwe wamutonza+ ndi kumunyoza? Ndi ndani amene iwe wamulankhula mokweza,+Ndiponso kumukwezera maso ako onyada? Ndi Woyera wa Isiraeli!+