Yesaya 6:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Aliyense ankauza mnzake kuti: “Woyera, woyera, woyera ndi Yehova wa magulu ankhondo akumwamba.+ Dziko lonse lapansi ladzaza ndi ulemerero wake.”
3 Aliyense ankauza mnzake kuti: “Woyera, woyera, woyera ndi Yehova wa magulu ankhondo akumwamba.+ Dziko lonse lapansi ladzaza ndi ulemerero wake.”