Ekisodo 2:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndiyeno wansembe wa ku Midiyani+ anali ndi ana aakazi 7. Iwo anafika pachitsimepo kuti atunge madzi ndi kuwathira momwera ziweto kuti ziweto za bambo awo zimwe. Ekisodo 18:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndiyeno Yetero, wansembe wa ku Midiyani, apongozi ake a Mose,+ anamva zonse zimene Mulungu anachitira Mose ndi anthu ake Aisiraeli komanso mmene Yehova anawatulutsira ku Iguputo.+
16 Ndiyeno wansembe wa ku Midiyani+ anali ndi ana aakazi 7. Iwo anafika pachitsimepo kuti atunge madzi ndi kuwathira momwera ziweto kuti ziweto za bambo awo zimwe.
18 Ndiyeno Yetero, wansembe wa ku Midiyani, apongozi ake a Mose,+ anamva zonse zimene Mulungu anachitira Mose ndi anthu ake Aisiraeli komanso mmene Yehova anawatulutsira ku Iguputo.+