-
Numeri 16:28, 29Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
28 Ndiyeno Mose anati: “Mudziwira izi kuti Yehova ndi amene wandituma kuti ndichite zonsezi, ndiponso kuti si zamʼmaganizo mwanga:* 29 Ngati anthuwa angafe mmene anthu onse amafera, ndiponso ngati chilango chawo chingakhale chofanana ndi chimene anthu onse amapatsidwa, ndiye kuti Yehova sananditume.+
-