2 Akorinto 8:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mogwirizana ndi zimene Malemba amanena kuti: “Munthu amene anali ndi zambiri sanali ndi zopitirira muyezo, ndipo munthu amene anali ndi zochepa sanali ndi zoperewera.”+
15 Mogwirizana ndi zimene Malemba amanena kuti: “Munthu amene anali ndi zambiri sanali ndi zopitirira muyezo, ndipo munthu amene anali ndi zochepa sanali ndi zoperewera.”+