Genesis 26:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Usiku umenewo, Yehova anaonekera kwa iye ndipo anamuuza kuti: “Ine ndine Mulungu wa bambo ako Abulahamu.+ Usaope,+ chifukwa ndili nawe. Ndidzakudalitsa ndi kuchulukitsa mbadwa* zako chifukwa cha Abulahamu mtumiki wanga.”+
24 Usiku umenewo, Yehova anaonekera kwa iye ndipo anamuuza kuti: “Ine ndine Mulungu wa bambo ako Abulahamu.+ Usaope,+ chifukwa ndili nawe. Ndidzakudalitsa ndi kuchulukitsa mbadwa* zako chifukwa cha Abulahamu mtumiki wanga.”+