Salimo 105:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kumbukirani ntchito zodabwitsa zimene wachita,Kumbukirani zozizwitsa zake ndi ziweruzo zimene wapereka,+ Salimo 105:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Anapempha nyama ndipo anawapatsa zinziri,+Ankawadyetsa chakudya chochokera kumwamba.+
5 Kumbukirani ntchito zodabwitsa zimene wachita,Kumbukirani zozizwitsa zake ndi ziweruzo zimene wapereka,+ Salimo 105:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Anapempha nyama ndipo anawapatsa zinziri,+Ankawadyetsa chakudya chochokera kumwamba.+