-
Numeri 13:26, 27Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
26 Iwo anabwerera kwa Mose ndi Aroni ndiponso gulu lonse la Aisiraeli mʼchipululu cha Parana, ku Kadesi.+ Anafotokozera gulu lonselo za ulendo wawo nʼkuwaonetsa zipatso za kudzikolo. 27 Iwo anauza Mose kuti: “Tinakalowa mʼdziko limene munatituma lija ndipo ndi dziko loyendadi mkaka ndi uchi,+ moti zipatso zake ndi izi.+
-