Deuteronomo 16:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Musankhe oweruza+ ndi atsogoleri a fuko lililonse mʼmizinda yonse imene* Yehova Mulungu wanu akukupatsani ndipo aziweruza anthu mwachilungamo. Deuteronomo 25:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 “Amuna akakangana azipita kwa oweruza,+ oweruzawo azigamula mlanduwo. Wolungama azimuweruza kuti alibe mlandu ndipo woipa azimuweruza kuti ali ndi mlandu.+
18 Musankhe oweruza+ ndi atsogoleri a fuko lililonse mʼmizinda yonse imene* Yehova Mulungu wanu akukupatsani ndipo aziweruza anthu mwachilungamo.
25 “Amuna akakangana azipita kwa oweruza,+ oweruzawo azigamula mlanduwo. Wolungama azimuweruza kuti alibe mlandu ndipo woipa azimuweruza kuti ali ndi mlandu.+